Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 29
5 Ine ndidzagona pansi nʼkupeza tulo,Ndipo ndidzadzuka ndili wotetezeka,Chifukwa Yehova akupitiriza kundithandiza.+