Salimo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma adzagwidwa ndi mantha aakulu,+Chifukwa Yehova ali pakati pa mʼbadwo wa anthu olungama.