Salimo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndi gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa+ komanso kapu yanga.+ Inu mumateteza cholowa changa. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, tsa. 25 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 29
5 Yehova ndi gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa+ komanso kapu yanga.+ Inu mumateteza cholowa changa.