Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:27 Nsanja ya Olonda,8/15/1986, tsa. 9
27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+