Salimo 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova atamandike,Chifukwa mʼnjira yodabwitsa, wandisonyeza chikondi chokhulupirika+ mumzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+
21 Yehova atamandike,Chifukwa mʼnjira yodabwitsa, wandisonyeza chikondi chokhulupirika+ mumzinda umene wazunguliridwa ndi adani.+