-
Salimo 37:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Iye adzachititsa kuti kulungama kwako kuwale ngati mʼmawa,
Ndipo chilungamo chako adzachichititsa kuti chiwale ngati dzuwa masana.
-