Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola malupanga awo ndipo akunga mauta* awo,Kuti agwetse oponderezedwa ndi osauka,Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zolungama.
14 Oipa asolola malupanga awo ndipo akunga mauta* awo,Kuti agwetse oponderezedwa ndi osauka,Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zolungama.