Salimo 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Yehova sadzasiya wolungama mʼmanja mwa woipayo+Kapena kumupeza wolakwa akamaweruzidwa.+