Salimo 39:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumathandiza munthu kuti asinthe pomupatsa chilango chifukwa cha zolakwa zake.+Mumawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete* imachitira. Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ (Selah)
11 Mumathandiza munthu kuti asinthe pomupatsa chilango chifukwa cha zolakwa zake.+Mumawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete* imachitira. Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ (Selah)