-
Salimo 44:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Chifukwa cha mawu a anthu amene akunditonza ndi kulankhula zachipongwe,
Ndiponso chifukwa cha mdani wathu amene akufuna kutibwezera zoipa.
-