Salimo 54:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu, imvani pemphero langa.+Tcherani khutu ku mawu ochokera mʼkamwa mwanga.