Salimo 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Inu Mulungu, munatikana ndipo munatigonjetsa.+ Munatikwiyira. Koma tsopano tiloleni tibwerere kwa inu.
60 Inu Mulungu, munatikana ndipo munatigonjetsa.+ Munatikwiyira. Koma tsopano tiloleni tibwerere kwa inu.