Salimo 61:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa inu Mulungu, mwamva malonjezo anga. Mwandipatsa cholowa chimene ndi cha anthu amene amaopa dzina lanu.+
5 Chifukwa inu Mulungu, mwamva malonjezo anga. Mwandipatsa cholowa chimene ndi cha anthu amene amaopa dzina lanu.+