Salimo 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzatalikitsa moyo wa mfumu,*+Ndipo idzakhala ndi moyo ku mibadwomibadwo.