Salimo 63:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+
5 Ndakhutira* ndi gawo labwino komanso losangalatsa kwambiri,*Choncho milomo yanga idzakutamandani pofuula mosangalala.+