Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa inu mumandithandiza,+Ndipo ndimafuula mosangalala mumthunzi wa mapiko anu.+