Salimo 66:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu onse padziko lapansi adzakugwadirani.+Adzaimba nyimbo zokutamandani,Adzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+ (Selah)
4 Anthu onse padziko lapansi adzakugwadirani.+Adzaimba nyimbo zokutamandani,Adzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+ (Selah)