Salimo 66:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tamandani Mulungu wathu, inu mitundu ya anthu,+Mutamandeni mofuula.