Salimo 66:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amene milomo yanga inalonjeza,+Ndiponso amene pakamwa panga pananena pa nthawi imene ndinali pamavuto aakulu.
14 Amene milomo yanga inalonjeza,+Ndiponso amene pakamwa panga pananena pa nthawi imene ndinali pamavuto aakulu.