Salimo 81:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Imvani anthu anga, ndipo ine ndipereka umboni wokutsutsani. Inu Aisiraeli, zikanakhala bwino ngati mukanandimvera.+
8 Imvani anthu anga, ndipo ine ndipereka umboni wokutsutsani. Inu Aisiraeli, zikanakhala bwino ngati mukanandimvera.+