Salimo 81:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iye adzakudyetsani tirigu wabwino kwambiri,*+Ndipo adzakupatsani uchi wochokera pathanthwe kuti mudye nʼkukhuta.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 81:16 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, tsa. 28
16 Koma iye adzakudyetsani tirigu wabwino kwambiri,*+Ndipo adzakupatsani uchi wochokera pathanthwe kuti mudye nʼkukhuta.”+