Salimo 101:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzachita zinthu mwanzeru komanso mosalakwitsa kanthu.* Kodi mudzandithandiza liti? Ndidzayenda mʼnyumba yanga ndi mtima wokhulupirika.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 101:2 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, tsa. 247/15/1998, tsa. 31
2 Ndidzachita zinthu mwanzeru komanso mosalakwitsa kanthu.* Kodi mudzandithandiza liti? Ndidzayenda mʼnyumba yanga ndi mtima wokhulupirika.+