Salimo 105:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Funafunani Yehova+ ndipo muzidalira mphamvu zake. Nthawi zonse muzimupempha kuti akuthandizeni.* Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 105:4 Nsanja ya Olonda,3/1/2000, tsa. 15