Salimo 107:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ankalamula kuti achire ndipo ankachiradi+Komanso ankawapulumutsa kuti asafe.