Salimo 107:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo apereke nsembe zoyamikira,+Komanso alengeze ntchito zake pofuula mosangalala.