Salimo 107:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+