Salimo 107:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chipululu amachisandutsa dambo la madzi,Ndipo dziko louma amalisandutsa dera la akasupe amadzi.+