Salimo 108:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.Ulemerero wanu ukhale padziko lonse lapansi.+