Salimo 108:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Popeza ndi woyera,* Mulungu walankhula kuti: “Ndidzasangalala popereka Sekemu+ ngati cholowa,Ndipo ndidzayezera anthu anga malo mʼchigwa cha Sukoti.+
7 Popeza ndi woyera,* Mulungu walankhula kuti: “Ndidzasangalala popereka Sekemu+ ngati cholowa,Ndipo ndidzayezera anthu anga malo mʼchigwa cha Sukoti.+