Salimo 108:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tithandizeni pamene tikukumana ndi mavuto,+Chifukwa chipulumutso chochokera kwa munthu nʼchopanda pake.+
12 Tithandizeni pamene tikukumana ndi mavuto,+Chifukwa chipulumutso chochokera kwa munthu nʼchopanda pake.+