Salimo 109:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova akumbukire zolakwa za makolo ake,+Ndipo tchimo la mayi ake lisafufutidwe.