-
Salimo 109:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iye anavekedwa matemberero ngati chovala.
Ndipo anathiridwa mʼthupi mwake ngati madzi,
Ndiponso mʼmafupa ake ngati mafuta.
-