Salimo 109:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amenewa ndi malipiro amene Yehova amapereka kwa amene amalimbana nane+Komanso kwa amene amalankhula zinthu zoipa zokhudza ine.
20 Amenewa ndi malipiro amene Yehova amapereka kwa amene amalimbana nane+Komanso kwa amene amalankhula zinthu zoipa zokhudza ine.