Salimo 109:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawondo anga akunjenjemera chifukwa chosala kudya,Ndawonda ndipo ndatsala mafupa okhaokha.*