-
Salimo 114:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Nanga inu mapiri, nʼchifukwa chiyani munkadumphadumpha ngati nkhosa zamphongo?
Inunso zitunda, nʼchifukwa chiyani munkadumphadumpha ngati ana a nkhosa?
-