Salimo 115:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akutikumbukira ndipo adzatidalitsa.Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli.+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.
12 Yehova akutikumbukira ndipo adzatidalitsa.Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli.+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.