Salimo 119:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chotsani zinthu zochititsa manyazi zimene ndikuziopa,Chifukwa zigamulo zanu ndi zabwino.+