Salimo 119:107 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 107 Ndavutika kwambiri.+ Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi mawu anu.+
107 Ndavutika kwambiri.+ Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi mawu anu.+