Salimo 130:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikuyembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.
6 Ndikuyembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.