Salimo 140:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene amakonza chiwembu mʼmitima yawo+Ndipo amayambitsa mikangano tsiku lonse.