Salimo 140:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, nditetezeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa anthu amene amachita zachiwawa.Amene amakonza chiwembu kuti andivulaze.
4 Inu Yehova, nditetezeni kuti manja a munthu woipa asandikhudze.+Nditetezeni kwa anthu amene amachita zachiwawa.Amene amakonza chiwembu kuti andivulaze.