Salimo 140:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndauza Yehova kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga. Mvetserani inu Yehova, kuchonderera kwanga kopempha thandizo.”+
6 Ndauza Yehova kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga. Mvetserani inu Yehova, kuchonderera kwanga kopempha thandizo.”+