Salimo 140:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, musapatse anthu oipa zimene amalakalaka. Musalole kuti ziwembu zawo zitheke kuti angayambe kunyada.+ (Selah)
8 Inu Yehova, musapatse anthu oipa zimene amalakalaka. Musalole kuti ziwembu zawo zitheke kuti angayambe kunyada.+ (Selah)