-
Miyambo 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Akanena kuti: “Tiye tipitire limodzi.
Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.
Tikabisale nʼkumadikirira anthu osalakwa kuti tiwaphe popanda chifukwa.
-