Miyambo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa mapazi awo amathamangira kukachita zoipa,Amapita mofulumira kukakhetsa magazi.+