Miyambo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Inu anthu osadziwa zinthu, kodi mukufuna kukhalabe osadziwa zinthu mpaka liti? Inu anthu onyoza, kodi mupitiriza kusangalala ndi kunyoza anthu mpaka liti? Ndipo anthu opusa inu, mudana ndi kudziwa zinthu mpaka liti?+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2022, ptsa. 19-21
22 “Inu anthu osadziwa zinthu, kodi mukufuna kukhalabe osadziwa zinthu mpaka liti? Inu anthu onyoza, kodi mupitiriza kusangalala ndi kunyoza anthu mpaka liti? Ndipo anthu opusa inu, mudana ndi kudziwa zinthu mpaka liti?+