Miyambo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukatero nyumba zako zosungiramo zinthu zidzadzaza kwambiri,+Ndipo zoponderamo mphesa zako zidzasefukira ndi vinyo watsopano. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,1/15/2000, tsa. 2512/15/1993, ptsa. 17-18
10 Ukatero nyumba zako zosungiramo zinthu zidzadzaza kwambiri,+Ndipo zoponderamo mphesa zako zidzasefukira ndi vinyo watsopano.