Miyambo 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova amatemberera banja la munthu woipa,+Koma iye amadalitsa nyumba ya munthu wolungama.+