Miyambo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Maso ako aziyangʼana patsogolo.Inde, uziyangʼanitsitsa* zinthu zimene zili patsogolo pako.+