Miyambo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa milomo ya mkazi wamakhalidwe oipa* imakha uchi ngati chisa cha njuchi,+Ndipo mʼkamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda,9/15/2006, tsa. 177/15/2000, ptsa. 28-29
3 Chifukwa milomo ya mkazi wamakhalidwe oipa* imakha uchi ngati chisa cha njuchi,+Ndipo mʼkamwa mwake ndi mosalala kuposa mafuta.+